Zimathandauza Chiani Kukhala Wa Nsembe
Kuchita Zinthu mu njira ya Yesu, (Mzuzu)
Mu bukhu la chibvumbulutso limati Yesu anatigula ife kukhala ufumu wa nsembe kutumikira Mulungu wathu (Chibvumbulutso 5) ngati tonse tingakhale ansembe tiyenera kudziwa kuti kukhala wansembe ndi chiani ngati tikufuna kukhala ndi mphamvu m’moyo mwathu tiyenera kukhala ndi maganizo a Mulungu pamoyo yathu. Yesu anati “pitani ndipo ndidzakhala nanu” Anatiphunzitsa, chitani chifuniro changa ndipo ndidzakupatsani inu moyo ndi mphamvu. Recorded: 29/8/1996
Download Entire MP3 Album | File size: 25.60MB
- Popanda maudindo – ndife tonse Asembe.
Play | Download | Length: 04:55 | File size: 1.5MB - Kutumukira anthu ndi kuthandiza wina ndi mnzake kukhala Yesu!
Play | Download | Length: 11:14 | File size: 3.31MB - Kuthetsa Mabvuto
Play | Download | Length: 14:54 | File size: 4.36MB - Chida chodabwitsa
Play | Download | Length: 08:59 | File size: 2.66MB - Nyimbo (1)
Play | Download | Length: 01:31 | File size: 0.52MB - Bwelani Mudzapeleke
Play | Download | Length: 05:51 | File size: 1.76MB - Musakwirire Luntha lanu
Play | Download | Length: 15:33 | File size: 4.54MB - Afunseni kuti akhale Ansembe (gawo lo yamba)
Play | Download | Length: 02:14 | File size: 0.73MB - Nyimbo (2)
Play | Download | Length: 04:21 | File size: 1.34MB - Afunseni kuti akhale Ansembe (gawo lo chiwiri)
Play | Download | Length: 05:17 | File size: 1.6MB - Pamene Yesu ali——————chimo silingakhale
Play | Download | Length: 08:13 | File size: 2.44MB - Nyimbo (3)
Play | Download | Length: 02:36 | File size: 0.83MB