YESU-KRISTO WOWONA … WOSATI ONAMA

ZOONA… OSATI OYELEKEZA, MUTU … OSATI ZOPEKA.

Kuitana kwa Mulungu ku dziko lapansi ndiyo malo pamodzi ndi Atate, Mwana ndi Mzimu Woyera—kukhala mkwatibwi wokonzeka kubwera kwa mkwatibwi wokongolayo, Yesu. (Yohane 13:15, Aefeso 2-5, Chibvumbulutso 19-7) ngati mukuganiza za chithunzi cha malembo mmene moyo, wa, kristu umakomanilana—uli bwanji? yofunsilana—ndi madyelero a ukwati Mulungu atifunsa ife, ati, “ Ndili nacho chiyembekezo ine. Ngati ukhala ndi ine, yanganila kuti ndine yani, palibenso wina ofanana nane. Palibe padziko lapansi amene adzakwanilitse moyo wako monga: ine—chifukwa ndinakulenga wa ine. Zina ndi zonse ndi zochotsera iwe, koma ngati ungathe kulowera mbali yanga, udzaona mmene moyo umayenela, ndipo tidzakhala pa ukwati.” “ Konzeka Mkwatibwi” 4/8/2007

    Chapters

  1. KONZEKERA WEKHA NAMWALI IWE!
  2. YESU: Omanga ndi Mmisili
  3. KUMANGA NDI MILIMO
    MPINGO NDI CHIANI NDI MKRISTO?
  4. KUMANGA NDI MAPANGIDWE NDI MAMANGIDWE A
    MOYO WA TSIKU NDI TSIKU PAMODZI
  5. KUMANGA KUTI IKHALE YA MPHAMVU
    KULIMBIKA MTIMA KUTI TISINTHE
  6. YESU: MTSOGOLERI NDI MUTU
  7. UTSOGOLERI WA YESU
    PA ANTHU AKE ONSE
  8. UTSOGOLERI WA YESU
    SAMUEL NDI SAULI
  9. UTSOGOLERI WA YESU
    MU MSONKHANO
  10. UTSOGOLERI WA YESU
    MU MOYO
  11. FUNILO LA MULUNGU…TSOPANO
 

Munkhoza kuchulukitsa bukhu loseli mutafunsa kwa mkozi ndipo muli ndi ufulu ochulukitsa monga lili bukhuli, koma bukhuli ndi losagulitsa pa mtengo uli wonse. (2 Akorinto 2:17 Mateyu 10:8)

©1985-2010 Haki Zote Zimehifadhiwa. Vitabu vyote na sauti zinapatikana bila malipo, kama zawadi kwa Yesu na wale ambao watatoa maisha yao kwa ajiili Yake. Wasiliana nasi kwa anwani ya barua ?. Na Neema Yake na Uzima Wake uwe juu yako, unapovaa Jina Lake na Kutembea katika Njia Zake. P.O. Box 68309, Indianapolis, IN 46268 USA or Contact@HouseChurch.com.